Prayers & Meditations

Nyanja (Malawi/Zambia) · Bahá'u'lláh

Add range:

Short Obligatory Prayer

To be recited once in twenty-four hours, at noon.

Ndicitira umboni, O! Mulungu wanga, kuti munandirenga ine kuti ndikudziweni ndi kukupembedzani. Nditsimikiza pa nthawi ino, kufooka kwanga ndi kukula kwa mphamvu Zanu, kusauka kwanga ndi kulemera Kwanu. Palibe Mulungu wina koma Inu nokha, Wothandiza pa tsoka, Wodzithandiza Nokha.