Prayers & Meditations
Nyanja (Malawi/Zambia) ·
Short Obligatory Prayer
To be recited once in twenty-four hours, at noon.
Ndicitila umboni, O Ambuye, Mulungu wanga, kuti munandilenga kuziwa Inu ndi kukondani Inu. Ndibvomela panthawi ino kulefuka kwanga ndi kukula kwa mphamvu zanu, kusauka kwanga ndi kulemela kwanu. Kulibenso Mulungu wina koma Inu nokha Muchinjilizi, Mwini zonse.